Mawu a M'munsi
a Makolo ambiri aona kuti buku la Phunzirani kwa Mphunzitsi Waluso, lofalitsidwa ndi Mboni za Yehova, n’lothandiza kwambiri pophunzitsa ana aang’ono za kugonana ndi mfundo zofunika za makhalidwe abwino pang’onopang’ono.