Mawu a M'munsi
a Kwa Akristu, kuchitidwa opaleshoni yokongoletsa thupi ndi nkhani ya munthu mwini payekha. Komabe, pali zinthu zofunika kwambiri zimene ayenera kuganizira. Kuti mumve zambiri, onani Galamukani! ya September 8, 2002, masamba 16-18.