Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO

Mawu a M'munsi

a Nkhani yakuti, “Achinyamata Akufunsa Kuti . . . Kodi Mnyamata Ndingamuuze Bwanji Kuti Ndikumufuna?” (November 8, 2004) inafotokoza kuti m’mayiko ena zingakhale zosemphana ndi chikhalidwe chawo kuti mkazi auze mwamuna kuti akumufuna chibwenzi. Ngakhale kuti Baibulo sililetsa akazi kufunsira amuna, limalimbikitsa Akristu kupewa kukhumudwitsa anthu ena. Choncho atsikana amene akufuna kuti Mulungu awadalitse afunika kuganizira malangizo a m’Baibulo akamaganizira zoti achite pa nkhani imeneyi.—Mateyu 18:6; Aroma 14:13; 1 Akorinto 8:13.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena