Mawu a M'munsi
b Kumapeto kwa milungu iwiri yoyambirira ya m’mwezi wa April 1951, akuluakulu a boma la Soviet Union anagwira mwadongosolo Mboni za Yehova zopitirira 7,000 ndi mabanja awo zomwe zinali kukhala kumadzulo kwa dziko la Soviet Union n’kuzikweza sitima kuyenda nazo ulendo wa makilomita ambiri kuzisamutsira ku dziko la Siberia.