Mawu a M'munsi
a Tiyenera kukumbukira kuti mbali zina za Baibulo zinalembedwa m’mawu ophiphiritsira, kapena zizindikiro. (Chivumbulutso 1:1) Choncho sitingadziwe kuti kodi ndi zinthu ziti zotchulidwa m’maulosi amenewa zomwe zidzagwiritsidwedi ntchito, ndiponso zimene zili zophiphiritsira chabe.