Mawu a M'munsi
a Chifukwa chakuti dzuwa likamaomba, malo ena amatentha pamene ena amakhala ozizira, zimenezi zimachititsanso kuti madzi a m’nyanja ayambe kuyenda ndipo madzi otentha amapita ku malo ozizira n’kukatenthetsa madzi a kumeneko.