Mawu a M'munsi
a Pali mitundu itatu ikuluikulu ya kudalirana: kudalirana kumene zamoyo zonse ziwiri zimapindula; kudalirana kumene kumapindulitsa chamoyo chimodzi popanda kupweteketsa chamoyo chinacho; ndi kudalirana kumene chamoyo chimodzi chimapindula movulaza chamoyo chinzakecho. Mu nkhani ino tifotokoza zitsanzo za kudalirana kumene kumapindulitsa zamoyo zonse ziwiri.