Mawu a M'munsi
d Popeza kuti pa Intaneti simungathe kum’dziwa bwinobwino munthu amene mukukambirana naye, m’posavuta kukunamizani kuti munthuyo ndi wamkazi kapena wamwamuna koma pamene zoona zake zenizeni n’zakuti ndi mwamuna mnzanu kapena mkazi mnzanu.