Mawu a M'munsi
a Malingana ndi kafukufuku amene anachitika ku France, akuti anthu amene amadwala matenda a mtundu winawake wotupa chiwindi ndipo ndi zidakwa, amakhala pangozi yaikulu kwambiri yoti chiwindi chawo chikhoza kuuma poyerekezera ndi amene amadwala matendawa koma samwa kwambiri. Ndi bwino kuti amene ali ndi matendawa azimwa mowa wochepa kwambiri kapena asamamwe n’komwe.