Mawu a M'munsi
b Azimayi amene akuyamwitsa ayenera kudziwa kuti akamwa mowa, mowawo umakaunjikana mu mkaka m’mawere awo. Ndiponso, mowa umene umakhala mu mkakamo umakhala wambiri kuposa umene umakhala m’magazi, chifukwa mu mkakawo mumakhala madzi ambiri amene angasungunule mowawo kuposa amene ali m’magazi.