Mawu a M'munsi
c Malo opempherera amenewa ndi oyenereradi mwambo waukwati wa Mboni za Yehova. Mwambo wake umakhala wosafuna zambiri ndipo pamakhala nkhani yachidule ya mfundo za m’Baibulo zomwe ndi maziko a ukwati wabwino. Ndipotu, salipiritsa kuti munthu achite mwambowu mu Nyumba ya Ufumu.