Mawu a M'munsi
b Kudzivulaza n’kosiyana ndi kuboola thupi kapena kudzidinda chidindo. Nthawi zambiri anthu amaboola thupi kapena kudzidinda chidindo chifukwa chotsatira mafashoni osati chifukwa choti ali ndi vuto la m’maganizo. Onani Galamukani! ya August 8, 2000, tsamba 16 ndi 17.