Mawu a M'munsi
c Lemba la Levitiko 19:28 limati: “Musamadzicheka matupi anu chifukwa cha akufa.” Mwambo wachikunja umenewu, umene mwina cholinga chake chinali kusangalatsa milungu imene ankakhulupirira kuti imasamalira anthu akufa, ndi wosiyana ndi chizolowezi chodzivulaza chomwe tikuchifotokoza m’nkhani ino.