Mawu a M'munsi
b Pali mitundu itatu ya matenda a ALS imene ikudziwika. Mitundu yake ndi: Osatengera kumtundu (omwe ali ofala kwambiri), otengera kumtundu (pafupifupi anthu 5 mpaka 10 pa anthu 100 alionse odwala matenda amenewa amakhala oti anatengera kumtundu). Ndipo pali a ku Guam (anthu ambiri amene adwalapo nthendayi ndi a ku Guam ndi zilumba zina za m’nyanja ya Pacific).