Mawu a M'munsi
d Dzinali linatengedwa ku mawu a Chiarabu akuti “Jennat-al-Arif,” amene nthawi zina amamasuliridwa kuti “minda ya maluwa ya m’mwamba,” ngakhale kuti n’kutheka kuti kwenikweni amatanthauza “munda wa maluwa wa katswiri wa zomangamanga.”