Mawu a M'munsi
c Mungayeserere kunena zakukhosi kwanu pozilemba m’buku nthawi zina. Olemba Baibulo amene analemba masalmo anali anthu amene nthawi zina ankavutika maganizo kwambiri ndipo ankafotokoza kudandaula kwawo, mkwiyo wawo, kukhumudwa kwawo, ndi chisoni chawo polemba m’buku. Mwachitsanzo, mwina mungawerenge Masalmo 6, 13, 42, 55, ndi 69.