Mawu a M'munsi
d Nthawi zina munthu amadzivulaza chifukwa cha matenda enaake, monga kuvutika maganizo, matenda ochititsa munthu kusinthasintha zochitika, matenda olephera kudziletsa kuchita zinthu zinazake, kapena matenda ovutika kudya. Galamukani! silangiza anthu kuti atsatire njira yakutiyakuti ya chithandizo. Akristu ayenera kuonetsetsa kuti chithandizo chilichonse chimene akulandira sichikutsutsana ndi mfundo za m’Baibulo.