Mawu a M'munsi
e Magazini a m’mbuyomu a Galamukani! afotokozapo nkhani zokhudza zinthu zimene nthawi zambiri zimayambitsa kudzivulaza. Mwachitsanzo, onani nkhani zakuti “Kumvetsetsa Matenda a Maganizo” (January 8, 2004), “Kuthandiza Achinyamata Amene Akuvutika Maganizo” (September 8, 2001), ndi nkhani zonena za matenda ovutika kudya za mu Galamukani! ya February 8, 1999, komanso nkhani ya “Zimene Achinyamata Amadzifunsa” yakuti “Kholo Chidakwa—Kodi Ndingalake Motani?” (August 8, 1992).