Mawu a M'munsi
a Ngakhale kuti dzina loti London linachokera ku liwu la Chilatini lakuti Londinium, mawu awiri onsewa n’kutheka kuti anachokera ku mawu akuti llyn ndi din a chinenero cha mitundu ina yakale imene inkakhala ku derali. Mawuwa akawaphatikiza amatanthauza “tawuni [kapena, linga] la panyanja.”