Mawu a M'munsi
a Nthambi ya United Nations yotchedwa United Nations Educational, Scientific, and Cultural Organization (UNESCO) imaika pa m’ndandanda wake wa malo ofunika kwambiri padziko lonse, malo achilengedwe amene ali ofunika chifukwa cha maonekedwe ake, zamoyo zake, miyala ndi nthaka yake, kapena amene ali ndi phindu pa zasayansi.