Mawu a M'munsi
a Ndende ya Auschwitz inali ndi zigawo zitatu zikuluzikulu, Auschwitz I (ndende yaikulu), Auschwitz II (Birkenau), ndi Auschwitz III (Monowitz). Zambiri mwa nyumba zoipa kwambiri zomwe ankapheramo anthu ndi mpweya wa gasi zinali ku Birkenau.