Mawu a M'munsi b Yesu anaphunzitsa ophunzira ake kuti ‘azikonda adani awo,’ osati kudana nawo ndi kuwapha.—Mateyu 5:43-45.