Mawu a M'munsi
a Makomiti Omanga Achigawo amapangidwa ndi magulu a Mboni za Yehova a anthu ongodzipereka amene agwira ntchito yomanga ndi kukonzanso Nyumba za Ufumu kwa nthawi yaitali. Pali magulu pafupifupi 100 oterewa ku United States komanso pali ena ambiri padziko lonse lapansi.