Mawu a M'munsi
a Chifukwa chowasokoneza ndi matenda ena ndiponso chifukwa choti nkhani zambiri zonena za anthu odwala matenda a CFP sizifalitsidwa, sizikudziwika kuti ndi anthu angati kwenikweni amene amadwala matendawa. Akatswiri osiyanasiyana amati chaka chilichonse, anthu okwana 50,000 amadwala matendawa padziko lonse.