Mawu a M'munsi
a Zopereka zoti zigwire ntchito yapadera timaziyamikira. Komabe, zingakhale bwino ngati zoperekazo ziperekedwa ku thumba lothandiza pa ntchito yapadziko lonse ya Mboni za Yehova, chifukwa ndalama zimachotsedwa m’thumba limeneli n’kugwiritsidwa ntchito ngati pagwa zinazake zofunika kuchitapo kanthu.