Mawu a M'munsi
a Mawu oti “mngelo” amene amatanthauza “mthenga,” nthawi zina amatanthauza zambiri, kuphatikizapo zolengedwa zauzimu za Mulungu ndi anthu amene anali atumiki ake. Koma mu nkhani ino, tikunena za zolengedwa zauzimu zimene Baibulo limazitcha angelo.