Mawu a M'munsi
b Mukavutika maganizo, mukhoza kukhala otsimikiza kuti Yehova amakusamalirani mwa kusinkhasinkha za malemba ngati otsatirawa: Eksodo 3:7; Salmo 9:9; 34:18; 51:17; 55:22; Yesaya 57:15; 2 Akorinto 4:7; Afilipi 4:6, 7; 1 Petro 5:7; 1 Yohane 5:14.