Mawu a M'munsi
a M’malo osiyanasiyana padziko lapansi, Aromani amatchedwa Majipise, Maketano, Matsigoina, Matsigani, Matsigane. Maina amenewa amaonedwa kuti ndi onyoza. Mawu akuti Mromani, (ambiri, Aromani) omwe amatanthauza “munthu” pa chinenero chawo, ndi amene Aromani ambiri amadzitchulira. Magulu ena a anthu olankhula Chiromani amatchedwa ndi mayina ena, monga mmene alili Asinti.