Mawu a M'munsi
a Ngakhale kuti nthawi zina Mulungu walowererapo pa zochita za anthu, zochita zake sizikhala zochirikiza dongosolo la zinthu la masiku anoli. M’malo mwake zimakhala zokhudzana ndi kukwaniritsidwa kwa chifuniro chake.—Luka 17:26-30; Aroma 9:17-24.