Mawu a M'munsi
a N’zochititsa chidwi kuti pa chikuto cha Baibulo lokhala ndi malifalensi la New American Standard Bible lofalitsidwa mu 1971 panalembedwanso mawu ofanana ndi amenewa, akuti: “Sitinayamikire kapena kugwiritsira ntchito dzina la katswiri aliyense chifukwa tikukhulupirira kuti Mawu a Mulungu ayenera kusonyeza okha kuti ndi olembedwa bwino kapena ayi.”