Mawu a M'munsi
c Onani buku lotanthauzira mawu lakuti A Manual Greek Lexicon of the New Testament, lolembedwa ndi G. Abbott-Smith, ndi lakuti A Greek-English Lexicon lolembedwa ndi Liddell ndi Scott. Malinga ndi mabuku amenewa, ndi mabuku enanso odalirika, mawu a Chigiriki amene ali pamenepa amatanthauza “kuika mwadongosolo, kuika pamalo pake.”