Mawu a M'munsi
a Kale anthu ankayeza zinthu pogwiritsira ntchito mikono. Mkono umodzi unkakhala mlingo woyambira pachigongono kukafika kudzala zakumanja. Zikuoneka kuti, m’nthawi ya Aisrayeli, mkono umodzi unkakhala masentimita 44 ndi theka.