Mawu a M'munsi
a N’zovuta kuyesa kuchepetsa vuto la kutentha kwa derali, lobwera chifukwa cha kutentha kwa padziko lonse. Komabe, kuyambira panthawi imene malowa anasankhidwa ndi bungwe la World Heritage, n’kukhala nawo m’gulu la malo a zachilengedwe ochititsa chidwi, anthu ambiri a m’dziko la Belize alimbikitsidwa kugwira nawo ntchito yoteteza malowa.