Mawu a M'munsi
a Makolo asamathamangire kuletsa ana awo kukhala pa Intaneti koma aziona bwinobwino zinthu zimene ana awo amakonda kutsegula pa Intanetipo. Potero angawathandize anawo ‘kugwiritsa ntchito luntha lawo la kuzindikira.’ (Aheberi 5:14) Kuphunzitsa ana m’njira imeneyi kumawathandiza kwambiri akakula.