Mawu a M'munsi
a Mapwando awiri okondwerera masiku akubadwa amene amatchulidwa m’Malemba anali achikunja ndipo panachitika zoipa. (Genesis 40:20-22; Maliko 6:21-28) Komabe, Mawu a Mulungu amalimbikitsa kuti tizipereka mphatso mochokera pansi pamtima, osati chifukwa cha anthu ena kapena anzathu ayi.—Miyambo 11:25; Luka 6:38; Machitidwe 20:35; 2 Akorinto 9:7.