Mawu a M'munsi
a Chomera chingathe kubala zipatso ndi mungu wochokera ku duwa la chomera china kapena mungu wochokera ku duwa lake lomwe. Komabe mbewu ya chomeracho imakhala yathanzi ndiponso yopirira ngati mungu wachokera ku duwa la chomera china.