Mawu a M'munsi
a Nkhaniyi ikufotokoza zimene dokotola wa mano amachita poteteza mano. Koma ngati mukufuna kudziwa mmene inuyo mungatetezere mano anu, werengani nkhani yakuti “How You Can Protect Your Smile,” mu Galamukani! ya Chingelezi ya November 8, 2005.