Mawu a M'munsi
b Zifukwa zimene Mulungu walolera mavuto kuchitika kwakanthawi chabe, zafotokozedwa mwatsatanetsatane mu Galamukani! ya November 2006 pa mutu wakuti, “Kuyankha Funso Lovuta Kwambiri Loti ‘Chifukwa Chiyani?’” komanso mutu 11 wa buku lakuti Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni? zofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.