Mawu a M'munsi
a Mungapeze malangizo a m’Malemba okuthandizani kupirira ndi kuthana ndi mavuto amene amadza chifukwa cha imfa ya munthu amene munali kum’konda, komanso nkhani zatsatanetsatane zokhudza lonjezo la kuuka kwa akufa m’kabuku kakuti Pamene Munthu Amene Mumakonda Amwalira, kofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.