Mawu a M'munsi
a M’zaka za m’ma 1200, Papa Gregory IX anakhazikitsa lamulo limene buku lina lakuti New Catholic Encyclopedia limati ndi “lamulo loyamba lokhazikitsidwa ndi papa loti anthu asamagwiritsire ntchito njira za kulera.”