Mawu a M'munsi
b Mawu akuti zithunzi zolaula amatanthauza zithunzi zamaliseche zomwe cholinga chake ndicho kum’patsa munthu chilakolako chofuna kugonana. Nkhani zowerenga kapenanso mawu odzutsa chilakolalo angakhalenso m’gulu la zinthu zolaula.