Mawu a M'munsi
a Anthu ena amachita zachiwawa chifukwa chosokonekera mutu, makamaka m’mayiko amene anthu osokonekera mitu amaloledwa kuyenda okha m’misewu komanso amatha kukhala ndi zida. Iyi ndi nkhani yovuta, koma cholinga cha nkhani ino si kufotokoza zimenezi.