Mawu a M'munsi
c Magazini ino ndiponso inzake ya Nsanja ya Olonda, yakhala ikutchula za anthu amene kale ankachita zosokoneza koma anasintha chifukwa chophunzira choonadi cha m’Baibulo. Onani Galamukani! ya July 2006, tsamba 11 mpaka tsamba 13; ya October 8, 2005, tsamba 20 ndi 21, ndi Nsanja ya Olonda ya January 1, 2000, tsamba 4 ndi 5; ya October 15, 1998, tsamba 27 mpaka tsamba 29; ndiponso ya February 15, 1997, tsamba 21 mpaka 24.