Mawu a M'munsi
b Akhristu sayenera kuona kutukwana ngati nkhani yamasewera, chifukwa Baibulo limati: “Mawu alionse owola asatuluke pakamwa panu.” “Nthawi zonse mawu anu azikhala achisomo, okoleretsa ndi mchere.”—Aefeso 4:29; Akolose 4:6.