Mawu a M'munsi
a Kuti muone umboni wina wokhudza “masiku otsiriza,” werengani Galamukani! ya April 2007, masamba 8 mpaka 10, ndiponso Nsanja ya Olonda ya September 15, 2006 masamba 4 mpaka 7, ndi ya October 1, 2005, masamba 4 mpaka 7. Magazini onsewa ndi ofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.