Mawu a M'munsi
a Posachedwapa ku United States anapeza kuti chaka chimodzi chokha ndege zotenga anthu kumeneko zinayenda ulendo wa makilomita 11 biliyoni, ndipo pa maola 334,448 aliwonse pankachitika ngozi imodzi yokha.
[Chithunzi pamasamba 14, 15]
(Onani m’magazini yeniyeni kuti mumvetse izi)
MMENE AMADZIWIRA PAMENE PALI NDEGE YANU
Makina a mumlengalenga
☒
Makina a pansi Chipangizo Nyumba yamphepo Chipangizo
choulutsira choonetsera
mawu pawailesi ndege pakompyuta