Mawu a M'munsi
a Tasintha maina m’nkhani ino.
ZOTI MUGANIZIRE
◼ N’chiyani chingachititse kuti makolo anu asayambebe kukukhulupirirani ngakhale mutayesetsa kusonyeza kuti ndinu wokhulupirika?
◼ N’chifukwa chiyani kulankhulana ndi makolo anu kuli kofunika kuti makolo anu azikukhulupirirani?