Mawu a M'munsi
c Dzina lakuti Yehova n’losiyana ndi maina omulemekezera akuti Wamphamvuyonse, Mlengi, Mulungu ndiponso Ambuye. M’malemba oyambirira a Baibulo Lopatulika, dzinali limapezekamo pafupifupi maulendo 7,000. Mulungu anadzipatsa yekha dzina limeneli. Lemba la Eksodo 3:15 limati: “Yehova . . . ndi dzina langa nthawi yosatha.”