Mawu a M'munsi
a Anthu amene amakonda Mulungu ndi anthu anzawo samvera nyimbo zolimbikitsa udani, chiwerewere kapena chiwawa. Iwo samvetseranso nyimbo zolimbikitsa ndale kapena kupembedza konyenga.—Yesaya 2:4; 2 Akorinto 6:14-18; 1 Yohane 5:21.