Mawu a M'munsi
e Akatswiri amachenjezanso kuti m’posavuta kuti achinyamata adziphe ngati m’nyumba mwawo muli mankhwala oopsa kapena mfuti. Pankhani ya mfuti, bungwe lina linati: “Ngakhale kuti anthu ambiri amati mfuti zawo ‘n’zodzitetezera,’ ambiri mwa anthu amene amafa ndi mfuti amachita kudzipha. Ndipo nthawi zambiri mfutiyo sikhala yawo.”—American Foundation for Suicide Prevention